Tools
Singing in the Shadow of AIDS
Extended Music
Malawi | Tanzania | Kenya | Uganda

Malawi Field Recordings
Part of Document Malawi: An Impoverished Nation
Translations by Albert Chimwemwe Nyirongo
All links are in RealAudio. (Audio Help)

Lura Secondary School - Paulendo Gospel Singers

Tizamkuluska Pakupemphera - We Will Win Through Praying (Tumbuka)
Audio Listen

Yesu mtaski wane/ndimwe nyali yane fumu
Jesus my savior/You are my light

Kalonga wamutende/Nkhutemweska imwe
My king who loves peace/I love you very much

Wabwezi wame ndimwe panyengo yavisuzgo/Mumtende, mviyezgo/Nkhutemweska imwe
You are my friend in difficult times/In times of peace, temptations/I love you very much

Muside ine chara/Mkhalenge nane fumu/mchipakato chinu/Nkhutemweska imwe
Don't leave me behind/Take me/into your hands/I love you very much

Nadi nkumanyiska wakupwererera wose/Walanda wakulira/Nkhutemweska imwe
I really know he cares for everybody/Orphans are crying/I love you very much

Wabwezi wame ndimwe panyengo yavisuzgo/Mumtende, mviyezgo/Nkhutemweska imwe
You are my friend in difficult times/In times of peace, temptations/I love you very much


Nkhomboli Primary School - HIV Club Solo

Oh Azanga, Ndifuna Ndifunse - Oh My Friends, I Want to Ask (Chewa)
Audio Listen

Oh azanga, ndifuna ndifunse/Ndamva kuti Edzi/Edzi ndi chiyani?
Oh my friends, I want to ask/I heard of AIDS/What is AIDS?

Edzi ndi matenda omwe agwedeza dziko
AIDS is a disease which has shaken the world

Zambia agwedeza dziko/Malawi agwedeza dziko/Tanzania agwedeza dziko
Zambia is shaken by it/Malawi is shaken by it/Tanzania is shaken by it

Azibambo ambiri anamwali ndi matendawa/Azimayi ambiri anamwali ndi matendawa
More fathers have died of the disease/More mothers have died of the disease

Anyamata ndi asungwana bwerani tikambirane kugonjetsa nthenday
Boys and girls, let's discuss how to conquer the disease

Ndikulimbika maphunziro/Ana amasiye achuluka/Makolo awo anamwali ndi matendawa
Work hard on education/The number of orphans is going up/Their parents died of the disease


Nkhomboli Secondary School - HIV Club Choir

Abale Matenda a Edzi - My Friend, There is AIDS (Tumbuka)
Audio Listen

Abale matenda a Edzi/Abale agwedeza dziko
My friend, there is AIDS/My friend, it has shaken the world

Abale matenda a Edzi/Alibe mankhwala
My friend, there is AIDS/It has no cure

Ndayendayenda pa dziko lose ndayaza kuti mankhwala kulibe
I have moved around the whole world and I haven't found any cure

Abale matenda a Edzi/Abale agwedeza dziko
My friend, there is AIDS/My friend, it has shaken the world

Abale matenda a Edzi/Alibe mankhwala
My friend, there is AIDS/It has no cure

Masambiro Yapachanya - Quality Education (Tumbuka)
Audio Listen

Masambiro yapachanya ndicho chuma chithu/Masambiro yapachanya yakutaska Edzi
Quality education is our country's economy/Quality education prevents AIDS

Tawana tikumala chifukwa cha Edzi/Wapapi wakumala chifukwa cha Edzi
Children are dying because of AIDS/Parents are dying because of AIDS

Unduna ukulira imwe masambiro ghamara
The Ministry is crying, education has gone down

Boma likulira imwe chitukuko chamara
The Government is crying, development has gone down

Ipo tiyeni pamoza tikwezge masambiro yapachnaya yakutaska Edzi
So now let's all together improve our education because quality education prevents AIDS

Tighakanenge Mauzaghali - Say No to Sex (Tumbuka)
Audio Listen

Tighakanenge masugardad ise
Say no to sugardads

Ndise ma lawyers ghamachero ise
We are the lawyers of tomorrow

Tighakanenge mauzaghali ise
Say no to sex

Ndise watola nkhrani wamachero ise
We are the journalists of tomorrow

Tighakanenge masugardad ise
Say no to sugardads

Tikulire - We Are Crying (Tumbuka)
Audio Listen

Kwabwera Edzi nthenda yoopsa/nthenda yopanda mankhwala iyi
There is AIDS, a killer disease/the disease which has no cure

Tayendayenda maiko oase/osawapeza mankhwala a Edzi
I searched the whole world for the drug/but I cannot find any cure for AIDS

Tikulira oh ndi nthenda iyi/Usalire oh mphavu zinaliko
We are crying because of the disease/Don't cry, we can fight the disease

Apita mai ndi nthenda iyi/apita bambo ndi nthenda iyi
My mom has died of the disease/my dad has died of the disease

Ndasala ndekha ndikulira ndizatani makolo apita
I'm just alone crying, and what am I going to do? My parents have gone

Ndaphunzira oh za nthenda iyi/Ndaphunzira oh kupewa Edzi
I have learned of this disease/I have learned to prevent AIDS

[Spoken]

Usalire mwana wanga, maphunziro ndiye tsogolo lako ukasunga khosi nkanda woyela udzavala
Don't cry my child, education is your future

Taphunzira za matenda a Edzi/katengedwe kake kafalitsidwe kake ndi kapewedwe kake
We learned of the disease AIDS/how you can get it, how it is spread, how it is prevented


Phoka Youth Organization Choir

Mtundu Wathu Watha - Our Tribe is Gone (Chewa)
Audio Listen

Naziona, naziona, naziona mbale wanga/zachisoni mtundu wathu watha
We are sad, my friend/Our tribe is gone

Chiwerewere mbale wanga ndicho chiyanbi chotengela Edzi
Sex my friend, is the common way of life

Wakunudzi, wakutauni, wolenera, wasauka alise angatenge Edzi
People from the villages, towns - rich and poor people could get AIDS

Nyamunyamu - Take You Up (Tumbuka)
Audio Listen

Namwe anyamata mutondeka kuchikola/Edzi nthenda yizamunyamula
If you boys fail to abstain/the disease AIDS will take you up

Name asugwana mutondeka kuchikola/Edzi nthenda yizamunyamula
If you girls fail to abstain/the disease AIDS will take you up

Nyamunyamu Oye/Nyamunyamu Edzi nthenda yizamunyamula
It'll take you up/The disease AIDS will take you up

Name wadada…/Namwe wamama…
If you men/women fail to abstain/the disease AIDS will take you up